nya-x-nyanja_eph_text_ulb/01/03.txt

1 line
258 B
Plaintext

\v 3 \v 4 Mulungu ndi Tate wa Ambuye Yesu Kristu atamandiwe, wamene anatidalisa na daliso ili yonse ya mu muzimu mu malo yaku mwamba mwa Kristu. Mulungu anatisanka mwa eve kuchokela ku chiyambi cha ziko, kuti tinkale oyera ndipo balibe choipa pa manso pake.