1 line
360 B
Plaintext
1 line
360 B
Plaintext
\c 1 \v 1 Paulo, mutumiki wa Kristu Yesu mu chifunilo cha Mulungu, ku bantu boyela ba ku Aefeso, bokululupilika mwa Kristu Yesu. (Malembo yena ya Chi Giliki yalibe, Ku Efeso, koma kalata ioneka inatumiwa ku dera lameni li mu mapingo yasiyanasiyana, osati chabe mu Efeso). \v 2 Chisomo kwainu na mutendere kuchokela kwa Mulungu Tate watu ndi Ambuye Yesu Kristu. |