nya-x-nyanja_eph_text_ulb/06/17.txt

1 line
280 B
Plaintext

\v 17 Ndipo tengani chisote chachiulumuso na lupanga lwa Muzimu, lyamene luli ndi mau ya Mulungu. \v 18 Napempelo lonse ndi pempezero, pempelani ntawi zonse mu Muzimu. Mukusilizisa, muziyanganila na kulimba konse pamene mupeleka ma pempelo yanu pa banthu bonse boyera ba Mulungu.