Fri Nov 22 2019 17:44:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-11-22 17:44:44 +02:00
parent 682ea2963f
commit 9504cfbab7
3 changed files with 3 additions and 0 deletions

1
05/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Koma pamene chintu chaululidwa mu kuwunika, chimaonekela. \v 14 Chifukwa chonse chamene chionekela nikuwanika. Chomwecho chikambiwa, “wuka, iwe wogona, ndipo ima kuchoka ku imfa, ndipo Kristu azawala pa iwe.”

1
05/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Onani mushe mwamene muyendera osati monga balibe nzelu koma ngaba nzelu. \v 16 Mubwezelepo ntawi chifukwa masiku niyoipa. \v 17 Chomwecho, musankale bopusa, koma zibani chifunilo cha Ambuye.

1
05/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 \v 19 \v 20 \v 21 Musakolewe na vinyo, chifukwa ichi chipeleka kumachitidwe yotayika. Koma, nkalani ozula na Muzimu Oyera, kukambisana mu masalimu ndi ma himino ndi nyimbo za uzimu, kuyimba ndi kukomesera kwa Ambuye na mutima wanu onse, Ndikupeleka mayamiko pa zonse muzina la Ambuye Yesu Kristu kuli Mulungu Tate, na kunvelelana wina ndi muzake mukoyopa Kristu.