Fri Nov 22 2019 17:48:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
657209922c
commit
838bf741f6
|
@ -1 +1 @@
|
|||
\v 25 \v 26 \v 27 Bamuna, kondani bakazi banu, mwamene Kristu anakondela mupingo ndi kuzipeleka eka mumalo mwake pakuti akaupatule, anauwamya ndi ku usuka na manzi na mau, pakuti angazipase eka mupingo wa ulemelero, wopanda banga, kapena kwinya, kapena kanthu kotere, koma oyera ndiopanda chilema.
|
||||
\v 25 Bamuna, kondani bakazi banu, mwamene Kristu anakondela mupingo ndi kuzipeleka eka mumalo mwake pakuti akaupatule, \v 26 anauwamya ndi ku usuka na manzi na mau, \v 27 pakuti angazipase eka mupingo wa ulemelero, wopanda banga, kapena kwinya, kapena kanthu kotere, koma oyera ndiopanda chilema.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 28 Munjila imozi bamuna bafunika kukonda bakazi babo monga matupi yabo. Wamene akonda mukazi wake azikonda eka nae. \v 29 Chifukwa kulibe muntu wamene anazondapo tupi yake, koma amaidyesa bwino na kuzisunga bwino, monga mwamene Kristu adyesela na kusunga bwino mupingo, \v 30 chifukwa ise ndise ziwalo za tupi yake.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 31 \v 32 \v 33 "Chifukwa chaichi mwamuna azasiya tate wake ndi mayi wake ndipo azapatikizana ku mukazi wake, ndipo aba babiri bazankala tupi imozi.” Ichi chonadi chobisika nichikulu – koma nilikulankula pa nkani ya Kristu ndi mupingo. 33Komanso, aliyense pa inu afunika kukonda mukazi wake monga mwamene azikondela, na mukazi apase ulemu mwamuna wake.
|
Loading…
Reference in New Issue