diff --git a/01/09.txt b/01/09.txt new file mode 100644 index 0000000..2e90983 --- /dev/null +++ b/01/09.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 9 \v 10 Mulungu anachipanga chozibika kwaise kubisika kwa chifunilo chake, kupitila muli chamene china mukondwelesa, ndipo chamene analangiza mwa Kristu, naichi na pamakonzedwe yofikila ntawi, kuleta zintu zonse pamozi, zintu ku mwamba na pansi, pa mutu umozi, ndipo Kristu. \ No newline at end of file diff --git a/01/11.txt b/01/11.txt new file mode 100644 index 0000000..ea3c9e4 --- /dev/null +++ b/01/11.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 11 \v 12 Mwa Kristu tinasankiwa mu cholowa chake, kukonzewelatu kulingana na pulani ya uyo wamene asebenza zonse kupitila na kukondwela kwa chifunilo chake. Mulungu anatinsaka monga bo mupyana pakuti, ise bamene bali boyambila ku kulupila mwa Kristu, tinkale ba matandiwe pa ulemerelo wake. \ No newline at end of file diff --git a/01/13.txt b/01/13.txt new file mode 100644 index 0000000..97ece7a --- /dev/null +++ b/01/13.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 13 \v 14 Mwa Kristu, imwe namwe, pamene munanvela mau ya zoona, utenga wa chipulumuso chanu, munakulupilira mwa eve na kudindiwa na Muzimu Oyera wamene anakuchitani chipangano, wamene ndi chizindikilo cha kupyana kwatu panka chiomboledwe chazintu, kukutamandiwa kwa ulemelelo wake. \ No newline at end of file diff --git a/01/15.txt b/01/15.txt new file mode 100644 index 0000000..4244b8d --- /dev/null +++ b/01/15.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mwaichi, pamene ninanvela pa chikulupililo chanu mwa Ambuye Yesu na chikondi chanu cha banthu bonse ba Mulungu bo yera, sinaleka kukamba zikomo kwa Mulungu chifukwa chaimwe pamene nikukambani imwe mu mapempelo yanga. \ No newline at end of file