Fri Nov 01 2019 16:15:42 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-11-01 16:15:42 +02:00
parent 06124e4ebb
commit 72c364f592
1 changed files with 1 additions and 0 deletions

1
01/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mulungu ndi Tate wa Ambuye Yesu Kristu atamandiwe, wamene anatidalisa na daliso ili yonse ya mu muzimu mu malo yaku mwamba mwa Kristu. Mulungu anatisanka mwa eve kuchokela ku chiyambi cha ziko, kuti tinkale oyera ndipo balibe choipa pa manso pake mwa chikondi.