Fri Nov 22 2019 17:36:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
35b3c7c75d
commit
6506b19c46
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 17 Nichomwecho, nikamba ndipo nifotokoza paizi mwa Ambuye, kuti masaziyenda monga mwamene bakunja bamayendela, mu kupusa kwa mu mitu zabo. \v 18 Balinamudimu mu kuziba kwabo, nibochosewako ku umoyo wa Mulungu chifukwa chakusaziba kwamene kuli muli beve, chifukwa chamitima zabo zolimba. \v 19 Banankala balibe nsoni ndipo banazipeleka beka ku chiwelewele, ndipo bamachita machitidwe ya madoti mukuzikonda.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 20 Koma simwamene munapunzila pali Kristu. \v 21 Niziba kuti munanvela pali eve, ndipo muna punzisiwa mwa eve, monga mwamene chonadi chili mwa Yesu. \v 22 Munapunzisiwa kuchosa za mankalidwe yakudala, kuchosako munthu wakudala. Ni munthu wakudala wamene ali nabumambala chifukwa chazifunilo zake zo nyenga.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 23 Munapunzisidwa ku sukiwa muzimu wa maganizo yanu, \v 24 ndipo kuvala munthu wa sopano wopangiwa mu chionekele cha Mulungu – mukudera na kuyenera kwa zoona.
|
Loading…
Reference in New Issue