nya-x-nyanja_deu_text_reg/18/22.txt

1 line
244 B
Plaintext

\v 22 Imwe muzaziba utenga ngati Yehova akamba pamene muneneli akamba mu zina ya Yehova. Ngati icho chintu sichioneka kapena kuchitika, icho ndicho chintu chamene Yehova sanakambe ndipo muneneli anakamba mozikuza, ndipo simufunika kumuyopa eve.