nya-x-nyanja_deu_text_reg/01/20.txt

1 line
317 B
Plaintext

\v 20 Ine ninakamba naimwe, 'Mufunika kubwela ku lupili ya ziko ya Amori, chamene Yehova Mulungu wathu atipasa kwa ife. \v 21 Onani, Yehova Mulungu wanu akonza malo pasogogolo panu; yendani pamwamba, tengani malo, monga Yehova, Mulungu wa batate banu, akambila kwa imwe; simufunika kuyopa, kapena kunkala wokumudwa. '