Sat Oct 02 2021 15:18:48 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 15:18:48 +02:00
parent 3cbc756200
commit d70d51c8eb
5 changed files with 7 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 20 \v 21 Pamenepo otsalawo adzamva ndi kuopa, ndipo kuyambira pamenepo sadzapanganso choipa china chotere pakati panu. Maso anu asawamvere chisoni; moyo ulipira moyo, diso kulipa diso, dzino kulipa dzino, dzanja ndi dzanja, phazi ndi phazi.
\v 20 Pamenepo otsalawo adzamva ndi kuopa, ndipo kuyambira pamenepo sadzapanganso choipa china chotere pakati panu. \v 21 Maso anu asawamvere chisoni; moyo ulipira moyo, diso kulipa diso, dzino kulipa dzino, dzanja ndi dzanja, phazi ndi phazi.

1
20/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 20 \v 1 Mukapita kukamenyana ndi adani anu, ndipo mukaona akavalo, magaleta, ndi anthu ambiri kukuposa inu, musawaope; pakuti Yehova Mulungu wako ali ndi iwe, amene anakutulutsa m'dziko la Aigupto.

1
20/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 \v 3 \v 4 Pamene mufuna kumenya nkhondo, wansembe ayandikire ndi kuyankhula ndi anthu. Awawuze kuti, 'Tamverani Aisraeli, mukumenya nkhondo ndi adani anu. Mitima yanu isakomoke. Musaope kapena kunjenjemera. Musaope iwo. Pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye akupita nanu kukamenyera nkhondo pa adani anu ndi kukupulumutsani. '

1
20/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 20

View File

@ -292,6 +292,9 @@
"19-14",
"19-15",
"19-17",
"19-20",
"20-title",
"20-01",
"33-01",
"33-03",
"33-05",