Sat Oct 02 2021 15:26:49 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 15:26:49 +02:00
parent 3368fbf645
commit d14834c5e2
4 changed files with 6 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 \v 18 M'mizinda ya anthu awa amene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, musasunge chilichonse chopuma. Mukawawononge kotheratu: Ahiti, Aamori, Akanaani, Aperezi, Ahivi, ndi Ayebusi, monga Yehova Mulungu wanu anakulamulirani. Chitani izi kuti asakuphunzitseni kuchita chilichonse chonyansa, monga achitira milungu yawo. Mukachita, mudzachimwira Yehova Mulungu wanu.
\v 16 M'mizinda ya anthu awa amene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, musasunge chilichonse chopuma. \v 17 Mukawawononge kotheratu: Ahiti, Aamori, Akanaani, Aperezi, Ahivi, ndi Ayebusi, monga Yehova Mulungu wanu anakulamulirani. \v 18 Chitani izi kuti asakuphunzitseni kuchita chilichonse chonyansa, monga achitira milungu yawo. Mukachita, mudzachimwira Yehova Mulungu wanu.

1
20/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Mukazungulira mzinda kwa nthawi yayitali, pomenya nawo nkhondo kuti muulande, musawononge mitengo yake pomenyetsa nkhwangwa. Popeza ungadye izi, usamaidula. Pakuti kodi mtengo wakuthengo ndi munthu amene muyenera kuzingilira? \v 20 Mitengo yokha yomwe mukudziwa kuti si mitengo yoti mudye, mutha kuwononga ndi kudula; umanga misewu yomenyana ndi mzinda womenyana nawe, mpaka udzagwa.

1
21/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 21

View File

@ -302,6 +302,9 @@
"20-10",
"20-12",
"20-14",
"20-16",
"20-19",
"21-title",
"33-01",
"33-03",
"33-05",