Sun Oct 03 2021 09:42:29 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 09:42:30 +02:00
parent 8f47566c3b
commit c2ba7b47d5
4 changed files with 5 additions and 0 deletions

1
26/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Lero Yehova walengeza kuti inu ndinu anthu ake, monga adakulonjezani, ndi kuti muyenera kusunga malamulo ake onse, \v 19 ndipo adzakukhazikitsani pamwamba pa amitundu onse amene anawalenga; kulandira matamando, kutchuka, ndi ulemu. Mudzakhala anthu opatulidwa kwa Yehova Mulungu wanu, monga ananena.

1
27/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 27 \v 1 \v 3 Ndipo Mose ndi akulu a Israyeli analamulira anthu, nati, Sungani malamulo onse ndikuuzani lero, \v 2 tsiku lomwe muoloka Yordano kulowa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani, muzimanga Mulembe pa mawu onse a chilamulo chimenechi mukatha kuwoloka, kuti mukalowe mdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, dziko loyenda mkaka ndi uchi ngati Yehova. Mulungu wa makolo anu anakulonjezani.

1
27/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 27

View File

@ -385,6 +385,8 @@
"26-12",
"26-14",
"26-16",
"26-18",
"27-title",
"33-01",
"33-03",
"33-05",