Sat Oct 02 2021 21:46:30 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 21:46:30 +02:00
parent 7545b6636c
commit b94da0e7a2
4 changed files with 6 additions and 0 deletions

1
21/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Iwo ayenera kuuza akulu a mzinda wake kuti, 'Mwana wathuyu ndi wamakani ndiponso wopanduka; samvera mawu athu; ndi wosusuka ndi chidakwa. ' \v 21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wake azim'ponya miyala kuti afe. kuti muchotse choipacho pakati panu. Aisraeli onse adzamva izi ndi kuchita mantha.

1
21/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Ngati munthu wachita tchimo loyenera imfa ndipo waphedwa, ndipo iwe nkumupachika pamtengo, \v 23 ndiye kuti mtembo wake suyenera kugona usiku wonse pamtengowo. M'malo mwake, umuike m'manda tsiku lomwelo; chifukwa aliyense wopachikidwa ndi wotembereredwa ndi Mulungu. Muzimvera lamuloli kuti musadetse dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.

1
22/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 22

View File

@ -315,6 +315,9 @@
"21-13",
"21-15",
"21-18",
"21-20",
"21-22",
"22-title",
"33-01",
"33-03",
"33-05",