Fri Feb 26 2021 08:42:45 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
simonmuzgtama 2021-02-26 08:42:46 +02:00
parent c6b5d38fb5
commit 883825449f
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 30 Koma Sihoni, mfumu ya Heshboni, sanafune kuleka ife kupitila kuli eve; chifukwa Yehova Mulungu wanu anayumisa maganizo yakeanalimbisa na kupanga mutima wake kuimilila, kuti iye angagonjese mwa zanu mpavu, monga iye manje achita lelo. \v 31 Yehova anakamba kuli ine, 'Ona, Ine nayamba kupulumusa Sihoni na malo yake basogolo panu; yambani kutenga, kuti imwe mutenge yake malo.'
\v 30 Koma Sihoni, mfumu ya Heshboni, sanafune kuleka ife kupitila kuli eve; chifukwa Yehova Mulungu wanu anayumisa maganizo yake na kulimbisa mutima wake, kuti iye angagonjese mwa zanu mpavu, monga iye manje achita lelo. \v 31 Yehova anakamba kuli ine, 'Ona, Ine nayamba kupulumusa Sihoni na malo yake basogolo panu; yambani kutenga, kuti imwe mutenge yake malo.'