From 861b86e0c5c2b6b0cdb18a08008d92de345b5b0c Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: simonmuzgtama Date: Wed, 6 Jan 2021 16:24:58 +0200 Subject: [PATCH] Wed Jan 06 2021 16:24:57 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 01/26.txt | 2 +- manifest.json | 3 ++- 2 files changed, 3 insertions(+), 2 deletions(-) diff --git a/01/26.txt b/01/26.txt index 9824c76..4141a83 100644 --- a/01/26.txt +++ b/01/26.txt @@ -1 +1 @@ -\v 26 \v 27 \v 28 Koma munakangiwa kugonjesa, koma munaukula mosusana na malamulo ya Yehoha wanu Mulungu. Munadandaula mu misasa yanu na kuti, ''Ni chifukwa kuti Yehova anatizonda ife kuti Iye abwelesa kwife kuchoka mu malo ya Igupto, kutipasa mukati mumanja ya Amori kutiononga ife. Nikuti kwamene tinga yende manje? Bathu babale bapanga yathu mitima kusungunika, kuti, 'Awo bathu ni bakulu na batali kuchila mwamene tilili; Minzi yawo ni ikulu ndipo niyochingiliziwa pamwamba kufika kumwamba; koma, tababona bana bamuna ba Anakimu \ No newline at end of file +\v 26 Koma munakangiwa kugonjesa, koma munaukula mosusana na malamulo ya Yehoha wanu Mulungu. \v 27 Munadandaula mu misasa yanu na kuti, ''Ni chifukwa kuti Yehova anatizonda ife kuti Iye abwelesa kwife kuchoka mu malo ya Igupto, kutipasa mukati mumanja ya Amori kutiononga ife. \v 28 Nikuti kwamene tinga yende manje? Bathu babale bapanga yathu mitima kusungunika, kuti, 'Awo bathu ni bakulu na batali kuchila mwamene tilili; Minzi yawo ni ikulu ndipo niyochingiliziwa pamwamba kufika kumwamba; koma, tababona bana bamuna ba Anakimu kuja.'' \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 4e447d1..7b92c3b 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -46,6 +46,7 @@ "01-17", "01-19", "01-20", - "01-25" + "01-25", + "01-26" ] } \ No newline at end of file