Sun Oct 03 2021 13:24:45 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 13:24:46 +02:00
parent ea6320f0b1
commit 48ebe081a0
5 changed files with 7 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Chifukwa chake mkwiyo wa Yehova wayakira dziko lino, kuti tibweretse matemberero onse olembedwa m'buku ili. Yehova wawazula m'dziko lawo mwaukali, ndi mkwiyo, ndi ukali waukulu, nawaponya m'dziko lina, monga lero.'
\v 27 Chifukwa chake mkwiyo wa Yehova wayakira dziko lino, kuti tibweretse matemberero onse olembedwa m'buku ili. \v 28 Yehova wawazula m'dziko lawo mwaukali, ndi mkwiyo, ndi ukali waukulu, nawaponya m'dziko lina, monga lero.'

1
29/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Zinthu zobisika ndi za Yehova Mulungu wathu yekha; koma zinthu zowululidwa ndizo zathu nthawi zonse ndi za zidzukulu zathu, kuti tichite mawu onse a chilamulo ichi.

1
30/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 30 \v 1 \v 3 Zinthu zonsezi zikadzakugwerani, madalitso ndi matemberero amene ndakupatsani, ndipo mukawakumbukira pakati pa mitundu ina yonse kumene Yehova Mulungu wanu wakuthamangitsirani, \v 2 ndi pamene mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu. mverani mawu ake, kutsatira zonse ndikulamulira lero, iwe ndi ana ako, ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse; adzabweranso nadzakusonkhanitsani inu mwa mitundu yonse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.

1
30/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 30

View File

@ -446,6 +446,9 @@
"29-20",
"29-22",
"29-25",
"29-27",
"29-29",
"30-title",
"33-01",
"33-03",
"33-05",