Sun Oct 03 2021 13:44:50 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 13:44:51 +02:00
parent b56f1d847d
commit 3b8aa6e7b6
4 changed files with 5 additions and 0 deletions

1
31/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Ndipo kunali, atatha Mose kulemba mawu a chilamulo ichi m'buku, \v 25 analamulira Alevi akusenza likasa la chipangano la Yehova, nati, \v 26 Tengani buku ili la chilamulo, nuliike pambali pa likasa la chipangano la Yehova Mulungu wako, kuti likhale mboni yokutsutsani.

1
31/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Pakuti ndidziwa kupanduka kwako, ndi khosi lako lolimba; Taonani, ndili ndi moyo pamodzi ndi inu, lerolino, mwapikisana ndi Yehova; koposa bwanji ndikadzamwalira? \v 28 Sonkhanitsani akulu onse a mafuko anu ndi atsogoleri anu, kuti ndiyankhule mawu awa m andmakutu mwawo ndi kuyitana kumwamba ndi dziko lapansi kuti zikhale mboni zotsutsana nawo. \v 29 Pakuti ndikudziwa kuti ndikadzamwalira mudzadziwononga nokha ndi kupatuka panjira imene ndakulamulirani; tsoka lidzafika pa iwe m'masiku otsatira. Izi zidzachitika chifukwa mudzachita zoipa pamaso pa Yehova ndi kumukwiyitsa ndi ntchito ya manja anu. ”

1
31/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Ndipo Mose ananena mawu a nyimbo iyi m'makutu a khamu lonse la Israyeli, kufikira adatha.

View File

@ -470,6 +470,8 @@
"31-19",
"31-21",
"31-22",
"31-24",
"31-27",
"33-01",
"33-03",
"33-05",