Sun Oct 03 2021 14:12:54 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 14:12:55 +02:00
parent 8555dab933
commit 364d46082c
4 changed files with 5 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 46 Ndipo iye anati kwa iwo, Khazikitsani mumtima mwanu mawu onse amene ndakulamulirani lero, kuti muwauze ana anu asunge mawu onse a chilamulo ichi; \v 47 Pakuti uwu si kantu kang'ono kwa inu, chifukwa ndiwo moyo wanu;popeza ndi moyo wanu, ndi ichi mudzatalikitsa masiku anu m'dziko muoloka Yordano kulilandira.
\v 46 Ndipo iye anati kwa iwo, Khazikitsani mumtima mwanu mawu onse amene ndakulamulirani lero, kuti muwauze ana anu asunge mawu onse a chilamulo ichi; \v 47 Pakuti uwu si kantu kang'ono kwa inu, chifukwa ndiwo moyo wanu; popeza ndi moyo wanu, ndi ichi mudzatalikitsa masiku anu m'dziko muoloka Yordano kulilandira.

1
32/48.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 48 Tsiku lomwelo Yehova analankhula ndi Mose, nati, \v 49 Kwera pamwamba pa mapiri a Abarimu, phiri la Nebo, lili m'dziko la Moabu, moyang'anana ndi Yeriko, ukaone dziko la Kanani, kupereka kwa ana a Israeli kukhala awo.

1
32/50.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 50 Udzafera pa phiri limene ukukwera, ndipo udzayikidwa kuti ukakhale ndi abale ako, monga momwe Aisraeli mnzako anafera pa Phiri la Hori ndipo nayikidwa pamodzi ndi anthu ake. \v 51 Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire ine pakati pa Aisraeli pa madzi a Meriba ku Kadesi, m thechipululu cha Zini; chifukwa simunandilemekeza ndi kundipatsa ulemu pakati pa ana a Israyeli. \v 52 Pakuti udzawona dzikolo pamaso pako, koma sudzapitako, ku dziko limene ndilipatsa ana a Israyeli. "

View File

@ -502,6 +502,8 @@
"32-42",
"32-43",
"32-44",
"32-46",
"32-48",
"33-01",
"33-03",
"33-05",