1 line
351 B
Plaintext
1 line
351 B
Plaintext
|
\v 17 \v 18 \v 19 Ndiye kuti onse awiri, omwe akukangana, ayenera kuyimirira pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza omwe amatumikira masiku amenewo. Oweruza ayenera kufunsa mwakhama; onani, ngati mboniyo ili mboni yonyenga, ndipo yanenera mbale wake monama, mum'chitire monga anafuna kuchitira mbale wake; kuti muchotse choipacho pakati panu.
|