Tue Jan 15 2019 20:36:03 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-15 20:36:05 +02:00
parent 15ed4e3c0a
commit 4807f87d72
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 40 \v 41 \v 42 \v 43 Petro anabacosa panja bonse, anagwada pansi, nopemphela; nobwela upindimukila kuli thupi, anakamba ati, "Tabita, nyamuka." Anasegula menso yake, ndipo pamene anaona Petro ananyamuka nonkhala. Petro anamugwila kwanja nomunyamula; ndipo pamene anaitana okhulupilila na azimai ofedwa, nomupeleka kulibeve wamoyo. Iyi nkhani inazibika mu Yopa monse, ndipo banthu bambili anakhulupila mwa Ambuye. Cinabwela cacitika kuti Petro anakhala masiku ambiri mu Yopa na mwamuna ocedwa Simoni, bopanga vikumba.
\v 40 Petro anabacosa panja bonse, anagwada pansi, nopemphela; nobwela upindimukila kuli thupi, anakamba ati, "Tabita, nyamuka." Anasegula menso yake, ndipo pamene anaona Petro ananyamuka nonkhala. \v 41 Petro anamugwila kwanja nomunyamula; ndipo pamene anaitana okhulupilila na azimai ofedwa, nomupeleka kulibeve wamoyo. \v 42 Iyi nkhani inazibika mu Yopa monse, ndipo banthu bambili anakhulupila mwa Ambuye. \v 43 Cinabwela cacitika kuti Petro anakhala masiku ambiri mu Yopa na mwamuna ocedwa Simoni, bopanga vikumba.