nya-x-nyanja_2sa_text_reg/14/32.txt

1 line
484 B
Plaintext

\v 32 Abisalomu anayanka Yowabu kuti, ninatumiza mau kuli iwe kukamba kuti, "bwela kuti nikutume kuli mfumu kukamba kuti, "Nichani chamene nanachiokela ku Gesha? Sembe chankala chabwino kuti nikali kuja. Maje chaichi lekani nione chinso cha mfumu, elo ngati ndine wolakwa, lekani kuti benve bani paye."" \v 33 Pamene apo Yowabu anayenda kuli mfumu naku iuza. Pamene mfumu anitana Abisalomu, anabwela kwa mfumu naku belamisa pansi pamenso yamfumu, ndipo mfumu ina mupyopyosa Abisalomu.