nya-x-nyanja_2sa_text_reg/18/24.txt

1 line
377 B
Plaintext

\v 24 Manje Davide enzeli nkale pakati pongenela napo chokela pachiseko. Kamalonda anayenda pamwamba pa utenga wapa geti wa dippa naku nyamula menso yake Pamene analangana anaona mwamuna achita kufika, atamanga eka. \v 25 Kamalonda anakuwa naku uza mfumu, Kuchoa apo mfumu inakamba kuti, "Ngati ali eka, muli utenga mukamwa mwake. Wotamanga anabwela pafupi na mufupi namuzinda.