nya-x-nyanja_2sa_text_reg/18/12.txt

1 line
359 B
Plaintext

\v 12 \v 13 Mwamuna anamuyanka Yowabu kutu, "Ngankale kuti nalandila mashekele yali sausanda ya siliva, siningafikise kwanja yanga pa mwana wanfumu, chifukwa tanvela tonse pamene mfumu akulamulilani iwe, kulibe wamene azagwila munyamata Abisalomu.' Sembe naika umoyo wanga pa cha boza (ndiye kulib e chobisika kuchokela kuli mfumu). Sembe mwanilekelela ine."