nya-x-nyanja_2sa_text_reg/06/08.txt

1 line
255 B
Plaintext

\v 8 Davidi anakalipa chifukwa Yehova anamugwemba Uzza, ndipo anaitana zina ya malo yaja Perezi Uzza. Malo yaja yaitaniwa Perezi Uzza kufikila lelo. \v 9 Davidi anayopa Yehova siku ija. Anakamaba kuti, nanga nichani likasa ya Yehova inga bsele kuli ine?"