Tue Apr 20 2021 10:10:45 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2021-04-20 10:10:46 +02:00
parent f9f1c7cf20
commit 25c78f89db
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 32 \v 33 Pamene apa mu Cushiti anafka naku kamba kuti, "kuli utenga wabwino wa bwana wanga mfumu, popeza Yehova akubwezelani lelo kuchokela kuli bonse bamene bana ku nyamukilani." Chokonkapo mfumu anakamba kuli mu Cushiti kuti, "Nanga zili bwino namunyamata mungona Abisalomu?" Mu Cushiti anayanka kuti, "Badani ba bwana wanga mfumu, na bonse bamene bana kunyamukilani ku ononga imwe, bafunika kunkala monga mwamene uja munyamata alili." Kuchoka apo mfumu inankala nachisoni, nakuyenda ku malo pa mwamba pa geti naku lila maninigi pamene enzeli kuyenda analilia, "mwana wanga mwamuna, mwana wanga mwamuna Abisalomu! Bansembe nenze nafa ndine mumalo mwako, Abisalomu, mwana wanga mwamuna, mwamuna wanga mwamuna.
\v 31 Pamene apa mu Cushiti anafka naku kamba kuti, "kuli utenga wabwino wa bwana wanga mfumu, popeza Yehova akubwezelani lelo kuchokela kuli bonse bamene bana ku nyamukilani." \v 32 Chokonkapo mfumu anakamba kuli mu Cushiti kuti, "Nanga zili bwino namunyamata mungona Abisalomu?" Mu Cushiti anayanka kuti, "Badani ba bwana wanga mfumu, na bonse bamene bana kunyamukilani ku ononga imwe, bafunika kunkala monga mwamene uja munyamata alili." \v 33 Kuchoka apo mfumu inankala nachisoni, nakuyenda ku malo pa mwamba pa geti naku lila maninigi pamene enzeli kuyenda analilia, "mwana wanga mwamuna, mwana wanga mwamuna Abisalomu! Bansembe nenze nafa ndine mumalo mwako, Abisalomu, mwana wanga mwamuna, mwamuna wanga mwamuna.