Wed Mar 17 2021 13:09:19 GMT-0700 (Pacific Daylight Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-03-17 13:09:20 -07:00
parent 6745d00f25
commit 7491a658dd
3 changed files with 4 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Koma Elisha anali nkale munyumba mwake naba kulu bana naye. Mfumu anatuma mwamuna kuchoka pasogolo pake, koma pamene mtumiki anabwela kuli Elisha, anakamba kuli bakulu, "Onani uyu mwana wa muna wa paya atuma kuti atenga mutu wanga? Onani pamene mtumiki azabwela, valani chiseko, na kugwila naku vala chiseko. Kodi sikubveka kwamendo ya mbuye wake kumboyo kwake?" Pamene enzeli akali kukamba nabeve, mtumiki anabwela pansi kuli eve. Mfumu anakamba, "Onani, ku
\v 32 Koma Elisha anali nkale munyumba mwake naba kulu bana naye. Mfumu anatuma mwamuna kuchoka pasogolo pake, koma pamene mtumiki anabwela kuli Elisha, anakamba kuli bakulu, "Onani uyu mwana wa muna wa paya atuma kuti atenga mutu wanga? Onani pamene mtumiki azabwela, valani chiseko, na kugwila naku vala chiseko. Kodi sikubveka kwamendo ya mbuye wake kumboyo kwake?" Pamene enzeli akali kukamba nabeve, mtumiki anabwela pansi kuli eve. \v 33 Mfumu anakamba, "Onani, kuvutika uku kuchokela kuli Yahwe. Nichani chamene nizayembekezela Yahwe?"

1
07/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 7

View File

@ -120,6 +120,8 @@
"06-24",
"06-27",
"06-30",
"06-32",
"07-title",
"10-title",
"10-01",
"10-04",