Sun Oct 03 2021 10:58:38 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 10:58:39 +02:00
parent 89d1c0f133
commit 699e5d2286
5 changed files with 7 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 18 \v 19 \v 20 Ndipo kudatero monga munthu wa Mulungu adanena kwa mfumu, kuti, Nthawi ngati iyi chipata cha Samariya chidzakhala ndi miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, ndi muyeso umodzi wa ufa ndi sekeli. Woyang'anira wamkuluyo adayankha munthu wa Mulungu nati, "Onani, ngakhale Yehova atapanga mawindo kumwamba, kodi izi zingachitike?" Elisa adati, "Udzionera ndi maso ako, koma osadya kanthu." Izi nzimene zinamuchitikira, chifukwa anthu anamponda pachipata ndipo anamwalira.
\v 18 Ndipo kudatero monga munthu wa Mulungu adanena kwa mfumu, kuti, Nthawi ngati iyi chipata cha Samariya chidzakhala ndi miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, ndi muyeso umodzi wa ufa ndi sekeli. \v 19 Woyang'anira wamkuluyo adayankha munthu wa Mulungu nati, "Onani, ngakhale Yehova atapanga mawindo kumwamba, kodi izi zingachitike?" Elisa adati, "Udzionera ndi maso ako, koma osadya kanthu." \v 20 Izi nzimene zinamuchitikira, chifukwa anthu anamponda pachipata ndipo anamwalira.

1
08/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 8 \v 1 Tsopano Elisa analankhula ndi mkazi amene anaukitsa mwana wake wamwamuna. Iye anati kwa iye, "Nyamuka, pita ndi banja lako, ndipo ukakhale kwina kulikonse kumene ungathe, m'dziko lina, chifukwa Yehova wayitanitsa njala yomwe idzabwere m'dziko lino kwa zaka zisanu ndi ziwiri." \v 2 Ndipo mkaziyo anauka namvera mau a munthu wa Mulungu. Anapita ndi banja lake ndipo anakhala m ofdziko la Afilisiti zaka zisanu ndi ziwiri.

1
08/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Ndipo kunali, zitatha zaka zisanu ndi ziwirizi, mkaziyo \v 4 anabwerera kuchokera kudziko la Afilisti; ndipo ananka kwa mfumu kukam'pempherera nyumba yake ndi munda wake. Tsopano mfumu inali ikulankhula ndi Gehazi mtumiki wa munthu wa Mulunguyo kuti, "Chonde ndiuzeni zazikulu zonse zimene Elisa wachita."

1
08/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 8

View File

@ -132,6 +132,9 @@
"07-12",
"07-14",
"07-16",
"07-18",
"08-title",
"08-01",
"10-title",
"10-04",
"10-08",