nya-x-nyanja_2ch_text_reg/15/03.txt

1 line
386 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 3 \v 5 Tsopano kwa nthawi yaitali, Israyeli analibe Mulungu woona, wopanda wansembe wophunzitsa, ndiponso wopanda chilamulo. \v 4 Koma mmasautso awo anatembenukira kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi kumufunafuna, ndipo anamupeza. Mmasiku amenewo munalibe mtendere kwa iye wotuluka kapena amene ankalowa, chifukwa panali chipwirikiti chachikulu pa anthu onse okhala mdzikolo.