nya-x-nyanja_2ch_text_reg/15/01.txt

1 line
228 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\c 15 \v 1 Mzimu wa Mulungu unadza pa Azariya mwana wa Odedi. \v 2 Anatuluka kukakumana ndi Asa nkumuuza kuti: “Ndimvereni, Asa, ndi Ayuda onse ndi Benjamini: Yehova ali nanu pamene inu muli ndi iye. Musiyeni, adzakusiyani.