nya-x-nyanja_2ch_text_reg/09/03.txt

1 line
450 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 3 Pamene Mfumukazi yaku Seba inaona nzelu za Solomoni na nyumba yaufumu yamene anamanga, \v 4 vakudya pa tebulo yake, ponkala pa banchito bake, nchito za banchito bake na vovala vawo, omupelekela chiko na vovala vawo, na nsembe zoshoka zamene anapeleka ku [[Akatswiri ena amanena kuti mawu akuti “nsembe zopsereza zimene anapereka” mnjira ina anganene kuti, “chitunda chimene anakwerapo”.]] nyumba ya Yehova, munalibe na mpepo muli eve.