nya-x-nyanja_2ch_text_reg/13/19.txt

1 line
479 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 19 Abiya anathamangitsa Yerobiamu; anamlanda midzi: Beteli ndi midzi yake, Yeshana ndi midzi yake, ndi Efroni ndi midzi yake. \v 20 Yerobiamu sanakhalenso ndi mphamvu masiku a Abiya; Yehova anamkantha, nafa. \v 21 Koma Abiya anakhala wamphamvu; anadzitengera akazi khumi ndi anayi, nabala ana amuna makumi awiri mphambu awiri, ndi ana akazi khumi ndi asanu ndi mmodzi. \v 22 Nkhani zina zokhudza Abiya, zochita zake ndi mawu ake, zinalembedwa mbuku la mbiri ya mneneri Ido.