nya-x-nyanja_2ch_text_reg/10/16.txt

1 line
290 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 16 Aisrayeli onse ataona kuti mfumu sinawamvere, anthu anamuyankha nkunena kuti, "Kodi Davide ali ndi gawo lotani? Tilibe cholowa mwa mwana wa Jese! Aliyense wa inu abwerere ku hema wake, Israyeli. Tsopano onani kunyumba kwanu, David." Chotero Aisrayeli onse anabwerera ku mahema awo.