nya-x-nyanja_2ch_text_reg/11/22.txt

1 line
337 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 22 Rehobowamu anasankha Abiya mwana wa Maaka kukhala mtsogoleri, mtsogoleri pakati pa abale ake; anaganiza zomupanga kukhala mfumu. \v 23 Rehabiamu analamulira mwanzeru; Anabalalitsa ana ake onse aamuna mdziko lonse la Yuda ndi Benjamini kumizinda yonse yamalinga. Anawapatsanso chakudya chochuluka ndipo ankawafunira akazi ambiri.