nya-x-nyanja_2ch_text_reg/11/20.txt

1 line
412 B
Plaintext

\v 20 Pambuyo pa Mahalati, Rehobowamu anatenga Maaka, mwana wamkazi wa Abisalomu; Iye anamuberekera Abiya, Atai, Ziza ndi Selomiti. \v 21 Rehobowamu anakonda Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu koposa akazi ake onse ndi adzakazi ake onse (anatenga akazi khumi ndi asanu ndi atatu, ndi adzakazi makumi asanu ndi limodzi, nabala ana amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu, ndi ana akazi makumi asanu ndi limodzi).