nya-x-nyanja_2ch_text_reg/11/18.txt

1 line
210 B
Plaintext

\v 18 Rehobowamu anadzitengera mkazi: Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti, mwana wa Davide, ndi Abihaili, mwana wamkazi wa Eliyabu, mwana wa Jese. \v 19 Iye anamuberekera ana aamuna: Yeusi, Semariya ndi Zahamu.