nya-x-nyanja_2ch_text_reg/16/11.txt

1 line
314 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 11 Taonani, machitidwe a Asa, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, taonani, zalembedwa m'buku la mafumu a Yuda ndi Israeli. \v 12 Mchaka cha 39 cha ulamuliro wake, Asa anadwala matenda a mapazi ake. Ngakhale kuti matenda ake anali aakulu kwambiri, iye sanapemphe thandizo kwa Yehova, koma kwa ochiritsa okha.