nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/20.txt

1 line
343 B
Plaintext

\v 20 Hezekiya, mfumu, ndi Yesaya mwana wa Amozi, mneneriyo adapemphera chifukwa cha izi ndipo adafuulira kumwamba. \v 21 Yehova anatumiza mngelo, amene anapha amuna ankhondo, akazembe, ndi akapitawo a mfumu kumisasa. Natenepa Sanakeribu abwerera ku dziko yace na manyadzo. Atalowa m ofnyumba ya mulungu wake, ana ake ena anamupha ndi lupanga.