nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/02.txt

1 line
425 B
Plaintext

\v 2 Hezekiya ataona kuti Sanakeribu wabwera komanso kuti akufuna kumenyana ndi Yerusalemu, \v 3 anakambirana ndi atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo; adamuthandiza kutero. \v 4 Anthu ambiri anasonkhana pamodzi ndipo anaimitsa akasupe onse ndi mtsinje womwe unkayenda mkatikati mwa dzikolo. Adati, "Chifukwa chiyani mafumu aku Asuri abwera ndikupeza madzi ambiri?"