nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/01.txt

1 line
213 B
Plaintext

\c 32 \v 1 Zitatha izi ndi ntchito zokhulupirika izi, Sanakeribu, mfumu ya Asuri, adabwera nalowa mu Yuda. Anamanga misasa kuti akaukire mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, yomwe ankafuna kuti adzilande.