nya-x-nyanja_2ch_text_reg/31/09.txt

1 line
331 B
Plaintext

\v 9 Kenako Hezekiya anafunsa ansembe ndi Alevi za miluyo. \v 10 Azariya wansembe wamkulu wa mnyumba ya Zadoki anayankha kuti, “Kuyambira pamene anthu anayamba kubweretsa zopereka ku nyumba ya Yehova, tadya ndi kukhuta, ndipo tatsala ndi zotsala, pakuti Yehova wadalitsa anthu. Chomwe chatsala ndi kuchuluka kwakukulu uku kuno. "