nya-x-nyanja_2ch_text_reg/02/01.txt

1 line
496 B
Plaintext

\c 2 \v 1 Manje solomoni analamulila kuti bamange nyumba ya zina ya Yehova na kumananga nyumba ya ufumu mu ufumu wake. \v 2 Solomo anaika bamuna 70,000 bonyamula katundu, na bamuna 80,000 kuti bankale bojuba myala kumalupili, na bamuna 3,600 kuti bazibayanganila. \v 3 Pamene apo Solomo anatumiza mau kuli Hiramu mfumu ya ku Turo, kukamba kuti, “Monga mwamene munachitila na tate wanga Davide, pakumutumizila mitengo ya mkunguza kuti amange nyumba yonkalamo, imwe muchite so chabe na kuli ine.