This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.
\v 12 Yehosafati anakhala wamphamvu kwambiri. Anamanga mipanda yolimba kwambiri ndi mizinda yosungirako zinthu m’Yuda. \v 13 Anali ndi katundu wambiri m’mizinda ya Yuda, ndi asilikali—ankhondo amphamvu—m’Yerusalemu.