This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.
\v 10 Mantha a Yehova anagwera maufumu onse a maiko ozungulira Yuda, kotero kuti sanachite nkhondo ndi Yehosafati. \v 11 Afilisti ena anapatsa Yehosafati mphatso, ndi siliva ngati msonkho. Aarabu anam’bweretseranso nkhosa, nkhosa 7,700, ndi mbuzi 7,700.