nya-x-nyanja_2ch_text_reg/17/07.txt

1 line
476 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 7 Mchaka chachitatu cha ulamuliro wake, anatumiza akalonga ake, Beni-Haili, Obadiya, Zekariya, Netaneli ndi Mikaya kuti akaphunzitse mmizinda ya Yuda. \v 8 Pamodzi ndi Alevi: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya, ndi Tobi-Adoniya; ndi pamodzi nao panali Elisama ndi Yehoramu ansembe. \v 9 Anaphunzitsa mYuda, ali nalo buku la chilamulo cha Yehova; Iwo anayendayenda mmizinda yonse ya Yuda ndi kuphunzitsa pakati pa anthu.