nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/32.txt

1 line
453 B
Plaintext

\v 32 Nkhani zina zokhudza Hezekiya, kuphatikizapo ntchito zosonyeza kukhulupirika kwa pangano, mukuona kuti zinalembedwa m visionmasomphenya a mneneri Yesaya mwana wa Amozi, ndi m ofbuku la mafumu a Yuda ndi Israeli. \v 33 Hezekiya anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuyika m onmanda pa phiri la manda a zidzukulu za Davide. Ayuda onse ndi anthu okhala mu Yerusalemu anamulemekeza iye pa imfa yake. Manase mwana wake analowa ufumu m hismalo mwake.