nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/22.txt

2 lines
402 B
Plaintext

\v 22 Mwa njira imeneyi, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala mu Yerusalemu m'manja mwa Sanakeribu, mfumu ya Asuri, ndi m'manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo mbali zonse.
\v 23 Ambiri anali kubweretsa zopereka kwa Yehova ku Yerusalemu, ndi mphatso zamtengo wapatali kwa Hezekiya mfumu ya Yuda, kotero kuti anayamba kukwezeka pamaso pa anthu a mitundu yonse kuyambira nthawi imeneyo.