nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/11.txt

1 line
366 B
Plaintext

\v 11 Kodi Hezekiya sakusokeretsani inu, kuti akupere inu kuti mufe ndi njala ndi ludzu, pamene iye adzati kwa inu, Yehova Mulungu wathu adzatipulumutsa m'dzanja la mfumu ya Asuri? \v 12 Kodi Hezekiya ameneyu sanachotse malo ake okwezeka ndi maguwa ake ansembe, nalamulira Yuda ndi Yerusalemu kuti, 'Mupembedze pa guwa limodzi la nsembe, ndipo mufukize nsembe zanu'?