nya-x-nyanja_2ch_text_reg/32/05.txt

1 line
215 B
Plaintext

\v 5 Hezekiya analimba mtima ndipo anamanga khoma lonse limene linali litagumuka. Anamanga nsanja zazitali, komanso khoma lina kunja. Analimbitsanso Milo mu mzinda wa David, ndipo anapanga zida zambiri ndi zishango.