nya-x-nyanja_2ch_text_reg/25/16.txt

1 line
287 B
Plaintext

\v 16 China bwela pamene mneneli anali kukamba naye, mfumu inakamba naye, "Takuika kuti unkale mlangizi wa mfumu? Leka! Nichifukwa cha chani uzapiliwa?" Mwaicho mneneli anya leka nakukamba, "Niziba kuti Mulungu aganiza zokuwonongani chifukwa mwachita ivi na simunamvele malangizo yanga."